Mabungwe omenyera ufulu pa nkhani za ubeleki apempha adindo kukambilanabe za bill yolola amayi kutchotsa pakati
Amayi ndi asungwana ambiri akupitilira kutaya mimba pogwiritsa ntchito njira zosayenera ngakhale m’chitidwewu uli oletsedwa malinga ndi malamulo a dziko lino zomwe…